Yuda 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu amenewa ndiwo amayambitsa magawano,+ amachita zauchinyama,+ ndipo alibe mzimu wa Mulungu.+