Yuda 24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma ponena za Mulungu amene angathe kukutetezani+ kuti musapunthwe, ndiponso kukuikani opanda chilema+ pamaso pa ulemerero wake ndi chisangalalo chachikulu, Yuda Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24 Nsanja ya Olonda,3/15/2012, ptsa. 21-22
24 Koma ponena za Mulungu amene angathe kukutetezani+ kuti musapunthwe, ndiponso kukuikani opanda chilema+ pamaso pa ulemerero wake ndi chisangalalo chachikulu,