Chivumbulutso 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ‘Ndikudziwa ntchito zako,+ khama lako, ndi kupirira kwako, ndiponso kuti sungalekelere anthu oipa. Iwe unayesanso+ anthu amene amadzitcha atumwi+ pamene sanali atumwi, ndipo unapeza kuti ndi onama. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 33-34 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 11
2 ‘Ndikudziwa ntchito zako,+ khama lako, ndi kupirira kwako, ndiponso kuti sungalekelere anthu oipa. Iwe unayesanso+ anthu amene amadzitcha atumwi+ pamene sanali atumwi, ndipo unapeza kuti ndi onama.