Chivumbulutso 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘Komabe, kwa ena nonse amene muli ku Tiyatira, nonsenu amene mulibe chiphunzitso chimenechi, amene simudziwa chilichonse chokhudza zinthu zimene amazitcha “zinthu zozama za Satana,”+ ndikuti: Sindikusenzetsani katundu wina wolemera.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:24 Nsanja ya Olonda,9/15/2010, tsa. 275/15/2003, tsa. 16 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 51-52
24 “‘Komabe, kwa ena nonse amene muli ku Tiyatira, nonsenu amene mulibe chiphunzitso chimenechi, amene simudziwa chilichonse chokhudza zinthu zimene amazitcha “zinthu zozama za Satana,”+ ndikuti: Sindikusenzetsani katundu wina wolemera.+