6 Patsogolo pa mpando wachifumuwo, panali nyanja yoyera mbee! ngati galasi,+ yooneka ngati mwala wa kulusitalo.
Pakati m’pakati pa mpando wachifumuwo, ndiponso mouzungulira, panali zamoyo zinayi+ zokhala ndi maso ambirimbiri, kutsogolo ndi kumbuyo komwe.