Chivumbulutso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:11 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 4 Nsanja ya Olonda,12/1/2008, tsa. 3112/1/1999, ptsa. 10-11 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 81
11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+
4:11 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 4 Nsanja ya Olonda,12/1/2008, tsa. 3112/1/1999, ptsa. 10-11 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 81