Chivumbulutso 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo angelo+ onse anaimirira mozungulira mpando wachifumu, limodzi ndi akulu,+ ndi zamoyo zinayi zija.+ Ndipo onse anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, pamaso pa mpando wachifumuwo ndi kulambira Mulungu.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:11 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2021, tsa. 16 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 124
11 Pamenepo angelo+ onse anaimirira mozungulira mpando wachifumu, limodzi ndi akulu,+ ndi zamoyo zinayi zija.+ Ndipo onse anagwada ndi kuwerama mpaka nkhope zawo pansi, pamaso pa mpando wachifumuwo ndi kulambira Mulungu.+