Chivumbulutso 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako ndinamva phokoso kumwamba ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndiponso ngati phokoso la bingu lamphamvu. Phokoso ndinamvalo linali ngati la oimba amene akuimba motsagana ndi azeze awo.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:2 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 200
2 Kenako ndinamva phokoso kumwamba ngati mkokomo wa madzi ambiri,+ ndiponso ngati phokoso la bingu lamphamvu. Phokoso ndinamvalo linali ngati la oimba amene akuimba motsagana ndi azeze awo.+