Chivumbulutso 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo utsi wa kuzunzidwa kwawo udzafuka kwamuyaya.+ Amene anali kulambira chilombo ndi chifaniziro chake, ndiponso aliyense amene walandira chizindikiro+ cha dzina lake, sadzapuma usana ndi usiku. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:11 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 210-211 Nsanja ya Olonda,4/15/1993, tsa. 7 Kukambitsirana, ptsa. 147-148
11 Ndipo utsi wa kuzunzidwa kwawo udzafuka kwamuyaya.+ Amene anali kulambira chilombo ndi chifaniziro chake, ndiponso aliyense amene walandira chizindikiro+ cha dzina lake, sadzapuma usana ndi usiku.
14:11 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 210-211 Nsanja ya Olonda,4/15/1993, tsa. 7 Kukambitsirana, ptsa. 147-148