Mawu Akumapeto
^ 2. Baibulo la Dziko Latsopano ndi losiyananso ndi Mabaibulo ena chifukwa limaperekedwa kwa anthu kwaulere. Zimenezi zikuthandiza kuti anthu ambiri aziwerenga Baibulo m’chinenero chawo. Baibuloli likupezeka m’zinenero 130 ndipo mukhoza kuwerenga kapena kulipanga dawunilodi pawebusaiti yathu ya www.pr2711.com.