Mawu a M'munsi Dzina lachiheberi lakuti “Seti” limatanthauza “Kusankhidwa; Kuika; Kukhazikitsa,” m’lingaliro la kulowa m’malo.