Mawu a M'munsi N’kutheka kuti mawu akuti “mzinda wa madzi” akutanthauza malo amene madzi a mumzindawo anali kuchokera.