Mawu a M'munsi Zikuoneka kuti amenewa ndi manda a Davide ndi mafumu a Yuda amene anabwera pambuyo pake.