Mawu a M'munsi M’Baibulo, mawu akuti “chitsiru” amatanthauza munthu amene amaphwanya dala mfundo za Mulungu.