Mawu a M'munsi “Chipini” ndi kachitsulo kapena kamtengo kokongoletsera kamene amakaika pabowo limene amaboola pamphuno.