Mawu a M'munsi “Msundu” ndi mtundu wa nyongolotsi zimene zimakhala m’madzi ndipo zimaluma anthu kapena zinyama n’kumayamwa magazi.