Mawu a M'munsi “Nalimata” ndi kabuluzi kakang’ono komwe kamakonda kukhala m’nyumba, koonekera matumbo.