Mawu a M'munsi Awa ndi malo okhawo m’buku la Nyimbo ya Solomo pamene pakupezeka dzina la Mulungu. Panopa, lalembedwa mwachidule kuti “Ya.” Onani mawu a m’munsi pa Eks 15:2 ndi Zakumapeto 1.