Mawu a M'munsi Pa Chiheberi vesi limeneli lili ngati kandakatulo kobwerezabwereza, kokhala ngati kanyimbo ka ana.