Mawu a M'munsi
M’Chiheberi mawu akuti “mtengo wa amondi” amatanthauza “wogalamuka” chifukwa chakuti ndi umodzi mwa mitengo yoyambirira kutulutsa maluwa. Izi zikugwirizana ndi mawu a Yehova pa vesi 12.