Mawu a M'munsi
Mkono umodzi ndi wofanana ndi masentimita 44 ndi hafu, ndipo “chikhatho” chinali masentimita 7.4. Kuphatikiza zimenezi zimakwana pafupifupi masentimita 51.8 ndipo zimaimira muyezo wotchedwa “mkono wautali.” Choncho bango loyezera la mikono 6 linali lalitali mamita 3.11.