Mawu a M'munsi Nʼkutheka kuti apa akunena za magazi amene anathiridwa paguwa lansembe. Magazi amenewa akuimira moyo.