Mawu a M'munsi
a Wonani pa Aefeso 5:3, 4, pamene mawu apatsogolo ndi apambuyo amapereka “kulankhula zopanda pake” ndi “zopusa” kukhala zosonya kuzakugonana. Chotero, mawu oipa ndi mawu opusa azakugonana saali a Akristu.