Mawu a M'munsi
b Amene kale anali dokotala wamkulu mu United States Dr. C. Everett Koop anayankha okayikira mwakuti: “Matenda a AIDS anayamba kulengezedwa m’dzikoli mu 1981. Tikanadziŵa pofika tsopano lino ngati AIDS imayambukira mwakukhudzana kwa nthaŵi zonse kosakhala kwa kugonana.”