Mawu a M'munsi
d Bungwe la U.S. Centers for Disease Control likupitiriza kuchenjeza kuti: “Ngati mufuna kukabooletsa makutu anu . . . , tsimikizirani kupita kwa munthu woyeneretsedwa amene amagwiritsira ntchito ziŵiya zatsopano kapena zotsukidwa m’mankhwala. Musachite manyazi kufunsa mafunso.”