Mawu a M'munsi
c Akatswiri ena amachenjeza kuti ngati mukakamiza ana anu kupsompsona kapena kukupatira munthu aliyense wofuna kusonyezedwa chikondi motero, mungawononge maphunziro ameneĊµa. Chotero, makolo ena amaphunzitsa ana awo kukana mwaulemu kapena kuchita mwanjira ina pamene wina awapempha kuchita zosayenera.