Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Nkhanza yogona mwana imachitika pamene wina agwiritsira ntchito mwana kukhutiritsa zilakolako zake zakugonana. Kaŵirikaŵiri kumaloŵetsamo zimene Baibulo limatcha dama, kapena por·neiʹa, imene imaphatikizapo kuseŵeretsa kumpheto, kugonana, ndi kugonana kwa kukamwa kapena kumatako. Machitidwe ena onyansa, monga kuseŵeretsa maŵere, kupereka malingaliro akugonana, kusonyeza zaumaliseche kwa mwana, kukonda kupenyerera kugonana kwa ena, ndi kusonyeza mpheto ena, zingakhale zimene Baibulo limatsutsa kukhala “kukhumba zonyansa.”—Agalatiya 5:19-21; onani Nsanja ya Olonda ya September 1, 1983, mawu amtsinde patsamba 30.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena