Mawu a M'munsi
a Ponena za mawu akuti “chimvero chonse” pa 1 Timoteo 2:11 (New International Version), wophunzira Baibulo W. E. Vine akuti: “Lamulolo silinali kunena za kulepa maganizo ndi chikumbumtima, kapena kuleka mathayo odzisankhira; mawu akuti ‘ndi kugonjera konse’ ali chenjezo loletsa kulanda ulamuliro, monga, mwachitsanzo, m’vesi lotsatira.”