Mawu a M'munsi
a Kuti mupeze chidziŵitso chonena za kusadalirika kwa kupima kwa carbon-14, onani Awake! ya September 22, 1986, tsamba 21, ndi Life—How Did It Get Here?—By Evolution or by Creation?, tsamba 96, zofalitsidwa ndi Watchtower Bible and Tract Society of New York, Inc.