Mawu a M'munsi
a Akatswiri a zamaphunziro a ukalamba aganizira njira zosiyanasiyana (zitaƔerengedwa nthaƔi ina, zinalipo zopitirira 300!) zimene zimalongosola mmene mwina ukalamba umachitikira. Komabe, njira zimenezi sizilongosola chifukwa chimene umachitikira.