Mawu a M'munsi
b Makomiti Olankhulana ndi Zipatala amaitananso ogwira ntchito m’zipatala ndi kuwasonyeza zina ndi zina. Kuphatikizanso apo, ngati achita kuitanidwa kuti adzathandizepo, iwo amathandiza odwala kuti alankhulane ndi dokotala wamkulu mwamsanga.