Mawu a M'munsi
a Mwa kutchula zimenezi, sitikunena za kuboola kolongosoka komwe n’kofala ndiponso kovomerezeka pachikhalidwe m’madera ambiri. Koma, tikunena za kuboola matupi konkitsa komwe n’kofala lerolino.—Onani Nsanja ya Olonda yachingelezi ya May 15, 1974, masamba 318-19.