Mawu a M'munsi
a Lipoti lakuti Not in the Public Interest—Local TV News in America (Zosapindulitsa Anthu—Nkhani za pa ma TV a mu America) ndi lachinayi pa kufufuza kwa pachaka kwa m’dziko lonselo kwa zinthu zimene zimakhala m’nkhani. Lipotili linalembedwa ndi Dr. Paul Klite, Dr. Robert A. Bardwell, ndi Jason Salzman, a Rocky Mountain Media Watch.