Mawu a M'munsi
a Pa nkhani imeneyi, mayiko ambiri amaletsa amuna kukwatiranso mkazi wina asanatenge kalata ya chilekaniro, kugonana pachibale, chinyengo, kuchitirana nkhanza m’banja ndiponso kukwatira kapena kukwatiwa udakali ndi zaka zochepa.