Mawu a M'munsi
a Makina oyezera zivomezi amayeza n’kusonyeza mmene nthaka ikugwedezekera kukamachitika chivomezi. Makina oyamba otere anapangidwa m’chaka cha 1890. Masiku ano, padziko lonse pali malo opitirira 4,000 oyezera zivomezi amene amagwiritsa ntchito makina otere.