Mawu a M'munsi
d Ngati simunafike msinkhu woloŵa m’banja, ndi bwino kucheza ndi amene si amuna kapena akazi anzanu muli pagulu. Onani nkhani yakuti “Achinyamata Akufunsa Kuti . . . Bwanji Ngati Makolo Anga Akuona Kuti Sindinafike Pokhala N’chibwenzi?” mu Galamukani! ya February 8, 2001.