Mawu a M'munsi a Mboni za Yehova zafalitsapo nkhani zimene zingathandize makolo pokambirana ndi ana awo za mankhwala osokoneza bongo. Mwachitsanzo, onani mutu 33 ndi 34 m’buku lakuti Mafunso Achichepere Akufunsa—Mayankho Amene Amathandiza.