Mawu a M'munsi
f Madokotala amati ndi bwino kuti anthu odwala matendaŵa aziyenda ndi khadi lowadziŵikitsa ndi kutinso azivala zinthu monga zibangili kapena mphete, zosonyeza kuti ali ndi matendaŵa. Zinthu zikafika poipa zimenezi zingathe kum’pulumutsa wodwalayo. Mwachitsanzo, madokotala angathe kusokonezeka n’kuchepa kwa shuga m’magazi n’kumaganiza kuti ndi matenda ena mwinanso kuti ndi uchidakwa.