Mawu a M'munsi
a Zaka zoposa 50 m’mbuyomu, bungwe la United Nations linayamba kutsatira mfundo za m’Chikalata cha Ufulu Wachibadwidwe. Gawo loyamba la mfundozo limati: “Anthu onse amabadwa omasuka ndipo amayenera kupatsidwa ulemu komanso ufulu wolingana.”