Mawu a M'munsi
b “Akuti kupopa mafuta kuchokera pa nsanja ya pamadzi yomwe aimanga pamtunda wopitirira mamita 300 pa nyanja ya Gulf of Mexico kumadya ndalama zochuluka pafupifupi maulendo 65 kuposa ndalama zimene zimafunika ku Middle East,” inatero The Encyclopædia Britannica.