Mawu a M'munsi
a Chifukwa chimodzi n’chakuti akazi amatha kukhala ndi vuto losokonezeka maganizo akabereka ndiponso thupi lawo limasintha akaleka kusamba. Chinanso n’chakuti, akazi sachita mphwayi kupita kuchipatala, motero matenda awo amadziŵika.