Mawu a M'munsi
c Madokotala amanena kuti nthaŵi zambiri, wodwala angathe kukhala woipidwa kwa miyezi ingapo ndithu kenaka n’kukhala wosangalala kwambiri kwa miyezi ina ingaponso. Komabe amati odwala ena amasintha nthaŵi zingapo ndithu pachaka. Mwa apo ndi apo, odwalawo amatha kusintha ngakhale pa maola 24 okha.