Mawu a M'munsi
a Kwenikweni mawuŵa amatanthauza kuti: “wokongola m’maso mwa Mulungu.” Malingana ndi buku lotchedwa The Expositor’s Bible Commentary, mawuŵa si kuti amangotanthauza maonekedwe otenga mtima a mwanayo komanso “mtima wake wabwino.”