Mawu a M'munsi
b Buku lolembedwa ndi Cook lija linati, “kusamba mumtsinje wa Nile kunali kofala ku Aigupto. Mtsinjewu anthu ankaulambira pokhulupirira kuti unkachokera . . . kwa mulungu wotchedwa Osiris, ndipo ankakhulupirira kuti madzi ake ali ndi mphamvu yopatsa moyo ndiponso yobereketsa.”