Mawu a M'munsi
e Akatswiri ena a mbiri yakale amati Farao amene ankalamulira pa nthaŵi imene Aisrayeli anali paulendo wawo wochoka ku Aigupto anali Thutmose Wachitatu. Ena amati anali Amenhotep II, enanso Ramses II ndi ena otero. Popeza kuti mzere wa mafumu a ku Aigupto n’ngosalongosoka bwinobwino, n’zosatheka kutsimikizira bwinobwino kuti Farao ameneyu anali ndani.