Mawu a M'munsi
b Ngati kusungulumwa sikukutha kwa nthaƔi yaitali kapena mukuganiza zodzipha, muyenera kufunafuna thandizo. Musachedwe, lankhulani ndi makolo anu kapena wachikulire wina amene mungamuululire zakukhosi.