Mawu a M'munsi a John Sinutko anakhalabe Mboni yokhulupirika ya Yehova mpaka imfa yake mu 1996 ali ndi zaka 92.