Mawu a M'munsi
c Muyenera kuganizira phindu limene mankhwalawo angabweretse limodzi ndi mavuto ena amene angabweretsenso. Magazini ya Galamukani! silangiza anthu kuti atsatire njira yakutiyakuti ya chithandizo. Akristu ayenera kuonetsetsa kuti chithandizo chilichonse chimene akutsatira sichikutsutsana ndi mfundo za m’Baibulo.