Mawu a M'munsi
a Mofanana ndi David, Mboni za Yehova zambiri zadzipereka kusamukira ku dera kumene kukufunika anthu ambiri olalikira za Ufumu, ndipo zina mwa izo zaphunzira chinenero chatsopano kuti ziphunzitse ena mfundo za choonadi zopezeka m’Mawu a Mulungu. Anthu odzipereka oterowo opitirira 400 panopa akutumikira ku Dominican Republic.