Mawu a M'munsi
a Lipotilo linali lotchedwa “Misinkhu Yoyenera Kuonerera Mapulogalamu Enaake, Ndiponso Kuteteza Ana” ndipo linalembedwa atachita kafukufuku amene anaphatikizapo ana a sukulu 340 a ku pulayimale limodzi ndi makolo awo ndi aphunzitsi awo.